Amuna anga anamwalira atavulazidwa ku tchito

Amuna anga anamwalira atavulazidwa ndi machine aku tchito. Pano aku office sakufuna kundithandiza ndipange bwanji