02 Feb Chitetezo cha ma alubino mu dela lathu lino ndichochepa Chitetezo cha ma alubino mu dela lathu lino ndichochepa. Kodi angatetetezeke bwanji
02 Feb Mwana wanga akulephela kupita ku sukulu Mwana wanga akulephela kupita ku sukulu akuwopa kumuba.
02 Feb Titani ndi munthu wokuba ma alubino Kodi tikapeza munthu akufuna kuba alubino titani? Tingakanene kuti?