Muno mu mudzi wa mfumu galawuza mukuchitika zodabwitsa. Mafumu akupeleka makobili kwa makolo a ana achitsikana ndi cholinga chowagulitsa atsinakanawa kwa alangizi azaumoyo amene akumayendela mu delali kwa miyezi yochepa.
Kodi malamulo a dziko lino akuti chani pa zimenezi? Kodi ndizololedwa? Tithandizeni ife anthu amu dela la galawuza timafunitsitsa kuti ana athu aphunzile ndipo asapange za banja. Timafuna atadzakhala atsogoleri amawa.