Amuna anga adachoka nyumba yomwe timakhala kukakhala pa rent, patatha mwezi adabwera ndi anthu kuzaona nyumba ija, ati awagulitsa nyumba yoti tinamanga tonse.
02
Feb