Mamuna wanga ananditumizira transport kuti ndibwere kuno ku town nditafika anazimitsa phone ndipo nditamupeza wandikana kuti sitingakhale limodzi pabanja koma ine ndili ndimwana wake.
23
May