Ndine tsikana waku mtandire ndipo ndakhala pabanja kwa zaka 4. Ine ndimamuna wanga banja linatha 2014 koma tili ndi ana awiri. Chodabwitsa ndichakuti dzana ndinapita ku show ya skefa koma ndisanalowe mamunayu anandipeza panja kuyamba kundimenya. Athu omwe anali pafupi anathawa chifukwa anayamba kumenya aliyese ofuna kuleletsa. Wandivulaza mpaka amafuna kundigwetsera muchitsime.
18
Oct