Ndine mzimayi waku area 25B. Mwana wa kwaneba wazaka 4 akumamugwirira mayike ake akachoka. Amayi ake amapanga uhule usiku, ndipo iwo amamusiya mwanayo nyumba yekha. Pakati pa usiku, azibambo osiyanasiyana amalowa nyumbamo ndikugona naye. Dzulo ndinamuyitana mwanayu kuti ndimusambitse ndipo sali bwino. Mungamuthandize bwanji?
06
Oct