Ndine mfumu yamu mdera laku mtandire. Kwathuku kunabwera khani yoti mwana wachichepere wazaka 16 wapera mimba kwa mtsikana wazaka 15. Athu akwa mtsikanayu amutenga mtsikanayu kukamutula kwa nyamatayo kuti akwatirane. Kodi mungawathandize bwanji anawa poti zaka zawo sizikuwayenereza kulowa banja.
21
Mar