02 Feb Kwa Neba dzulo kunali phokoso Kwa Neba dzulo kunali phokoso la zaoneni, abambo akumeneku akaledzela
02 Feb Amuna anga adachoka nyumba yomwe timakhala Amuna anga adachoka nyumba yomwe timakhala kukakhala pa rent
02 Feb Ufulu Wanga helped me break free I am thankful to Ufulu Wanga for their platform I am a happy single mother of two
04 Apr Amuna anga akumandizuza kamba ka mkazi wachiwiri Amuna anga anakwatira akazi achiwiri ndipo akumandizuza.
23 May Mamuna wanga akundikana Mamuna wanga ananditumizira transport kuti ndibwere kuno ku town nditafika anazimitsa phone
12 Jul Mamuna wanga akufuna kundikhwimira Ndine mzimayi wa ana atatu ndipo ndimakhala ku mtandire mu Mzinda wa Lilongwe. Mwamuna wanga amafuna kundidula maliseche ndi cholinga chopangira mankhwala kuti apeze chuma.
18 Oct Mamuna wanga wakale wandimenya mondivulaza Ndine tsikana waku mtandire ndipo ndakhala pabanja kwa zaka 4. Ine ndimamuna wanga banja linatha 2014 koma tili ndi ana awiri.