02 Feb Mwana wanga akulephela kupita ku sukulu Mwana wanga akulephela kupita ku sukulu akuwopa kumuba.
02 Feb Chitetezo cha ma alubino mu dela lathu lino ndichochepa Chitetezo cha ma alubino mu dela lathu lino ndichochepa. Kodi angatetetezeke bwanji
02 Feb Tikuthokoza kwa apolisi mu dela la zalewa Tikuthokoza kwa apolisi mu dela la zalewa, atamva zakubedwa kwa ana anatithandiza
02 Feb Tingadziwe bwanji kuti tikunamizidwa za kunja Tingadziwe bwanji kuti tikunamizidwa kapena ndi mwayi