25
Sep
20. Amuna anga anamwalira atavulazidwa ndi machine aku tchito. Pano aku office sakufuna kundithandiza ndipange bwanji