02 Feb Ndikwatire ndisanamalize sukulu Makolo anga akufuna ndikwatire ndisanamalize sukulu. Ine ndithawa.
02 Feb Mafumu akupeleka makobili kwa makolo Muno mu mudzi wa mfumu galawuza mukuchitika zodabwitsa. Mafumu akupeleka makobili kwa makolo a ana achitsikana